10 “Mundipangire Likasa la mtengo wa mthethe,+ mikono* iwiri ndi hafu m’litali, mkono umodzi ndi hafu m’lifupi, ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.
33 Chotero iwo ananyamuka kuphiri la Yehova,+ n’kuyenda ulendo wa masiku atatu. Likasa la pangano la Yehova+ linali patsogolo pawo ulendo wa masiku atatu wonsewo, kuwafunira malo oti amangepo msasa.+