Salimo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani kufuula kwanga kopempha thandizo,+Inu Mfumu yanga+ ndi Mulungu wanga, chifukwa ndimapemphera kwa inu.+ Yesaya 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atamva mawu amenewa, Hezekiya anatembenukira kukhoma+ n’kuyamba kupemphera kwa Yehova.+ Afilipi 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+
2 Imvani kufuula kwanga kopempha thandizo,+Inu Mfumu yanga+ ndi Mulungu wanga, chifukwa ndimapemphera kwa inu.+
6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+