Salimo 44:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu Mulungu, ndinu Mfumu yanga.+Lamulani kuti Yakobo alandire chipulumutso chachikulu.+ Salimo 74:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,+Iye ndiye wondipatsa chipulumutso chachikulu padziko lapansi.+ Salimo 145:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 145 Ndidzakukwezani, inu Mfumu ndi Mulungu wanga,+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Yesaya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+
12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,+Iye ndiye wondipatsa chipulumutso chachikulu padziko lapansi.+
145 Ndidzakukwezani, inu Mfumu ndi Mulungu wanga,+Ndipo ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+