1 Mafumu 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mumve pemphero lopempha chifundo+ la mtumiki wanu ndi la anthu anu Aisiraeli, limene angapemphere atayang’ana malo ano. Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ ndipo mumve n’kukhululuka.+ 2 Mafumu 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atamva mawu amenewa, Hezekiya anatembenukira kukhoma+ n’kuyamba kupemphera kwa Yehova+ kuti: Mateyu 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwe popemphera, lowa m’chipinda chako pawekha+ ndi kutseka chitseko, ndipo pemphera kwa Atate wako amene ali kosaoneka.+ Ukatero Atate wako amene amaona kuchokera kosaonekako adzakubwezera.
30 Mumve pemphero lopempha chifundo+ la mtumiki wanu ndi la anthu anu Aisiraeli, limene angapemphere atayang’ana malo ano. Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ ndipo mumve n’kukhululuka.+
6 Koma iwe popemphera, lowa m’chipinda chako pawekha+ ndi kutseka chitseko, ndipo pemphera kwa Atate wako amene ali kosaoneka.+ Ukatero Atate wako amene amaona kuchokera kosaonekako adzakubwezera.