1 Mafumu 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso, m’chipinda chamkati anapangamo akerubi+ awiri kuchokera ku mtengo wamafuta.* Kerubi aliyense anali mikono 10 kutalika kwake.+
23 Komanso, m’chipinda chamkati anapangamo akerubi+ awiri kuchokera ku mtengo wamafuta.* Kerubi aliyense anali mikono 10 kutalika kwake.+