1 Mafumu 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chipinda chamkati chinali mikono 20 m’litali, mikono 20 m’lifupi+ ndi mikono 20 kutalika kwake. Chipindacho anachikuta ndi golide woyenga bwino,+ komanso anakuta guwa lansembe+ ndi matabwa a mkungudza.
20 Chipinda chamkati chinali mikono 20 m’litali, mikono 20 m’lifupi+ ndi mikono 20 kutalika kwake. Chipindacho anachikuta ndi golide woyenga bwino,+ komanso anakuta guwa lansembe+ ndi matabwa a mkungudza.