2 Mbiri 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi si Hezekiya yemweyo amene anachotsa malo ake okwezeka+ ndi maguwa ake ansembe+ kenako n’kuuza anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti: “Muziwerama+ pamaso pa guwa lansembe limodzi lokha+ ndipo nsembe yautsi muzifukiza pamenepo”?+
12 Kodi si Hezekiya yemweyo amene anachotsa malo ake okwezeka+ ndi maguwa ake ansembe+ kenako n’kuuza anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti: “Muziwerama+ pamaso pa guwa lansembe limodzi lokha+ ndipo nsembe yautsi muzifukiza pamenepo”?+