Danieli 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Belisazara ataledzera ndi vinyoyo+ anaitanitsa ziwiya zagolide ndi zasiliva+ zimene Nebukadinezara bambo ake anatenga m’kachisi ku Yerusalemu. Anaitanitsa zimenezi kuti mfumuyo, nduna zake, adzakazi* ake ndi akazi ake ena apambali amweremo.+
2 Belisazara ataledzera ndi vinyoyo+ anaitanitsa ziwiya zagolide ndi zasiliva+ zimene Nebukadinezara bambo ake anatenga m’kachisi ku Yerusalemu. Anaitanitsa zimenezi kuti mfumuyo, nduna zake, adzakazi* ake ndi akazi ake ena apambali amweremo.+