1 Mbiri 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 golide wopangira zinthu zagolide, siliva wopangira zinthu zasiliva, ndi siliva woti amisiri adzagwirire ntchito zonse. Ndani lero ali wokonzeka kupereka mphatso kwa Yehova?”+ Ezara 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ine ndaika lamulo+ lakuti aliyense mu ufumu wanga+ pakati pa anthu a Isiraeli, ansembe awo, ndi Alevi amene akufuna kupita nawe ku Yerusalemu apite.+
5 golide wopangira zinthu zagolide, siliva wopangira zinthu zasiliva, ndi siliva woti amisiri adzagwirire ntchito zonse. Ndani lero ali wokonzeka kupereka mphatso kwa Yehova?”+
13 ine ndaika lamulo+ lakuti aliyense mu ufumu wanga+ pakati pa anthu a Isiraeli, ansembe awo, ndi Alevi amene akufuna kupita nawe ku Yerusalemu apite.+