1 Mafumu 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 inuyo mumve muli kumwamba ndipo mukhululuke tchimo la atumiki anu, anthu anu Aisiraeli, popeza mumawaphunzitsa+ njira yabwino yoti ayendemo.+ Mubweretse mvula+ padziko lanu, limene mwapatsa anthu anu monga cholowa.
36 inuyo mumve muli kumwamba ndipo mukhululuke tchimo la atumiki anu, anthu anu Aisiraeli, popeza mumawaphunzitsa+ njira yabwino yoti ayendemo.+ Mubweretse mvula+ padziko lanu, limene mwapatsa anthu anu monga cholowa.