1 Mafumu 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Patapita masiku ambiri,+ mawu a Yehova anafikira Eliya m’chaka chachitatu, kuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula padziko lapansi.”+ Salimo 68:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Mulungu, munayamba kugwetsa mvula yamphamvu,+Ngakhale pamene anthu anu anali ofooka, inu munawalimbitsa.+
18 Patapita masiku ambiri,+ mawu a Yehova anafikira Eliya m’chaka chachitatu, kuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula padziko lapansi.”+
9 Inu Mulungu, munayamba kugwetsa mvula yamphamvu,+Ngakhale pamene anthu anu anali ofooka, inu munawalimbitsa.+