Levitiko 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 m’mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova chikondwerero cha misasa kwa masiku 7.+ Deuteronomo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Uzichita chikondwerero cha misasa+ masiku 7, potuta zokolola kuchokera pamalo opunthira mbewu, pamalo oyengera mafuta ndi pamalo opondera mphesa.
34 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 m’mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova chikondwerero cha misasa kwa masiku 7.+
13 “Uzichita chikondwerero cha misasa+ masiku 7, potuta zokolola kuchokera pamalo opunthira mbewu, pamalo oyengera mafuta ndi pamalo opondera mphesa.