2 Samueli 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Hiramu+ mfumu ya Turo anatumiza amithenga+ kwa Davide. Anatumizanso mitengo ya mkungudza,+ anthu a ntchito zamatabwa ndi a ntchito za miyala yomangira khoma,* ndipo anayamba kumanga nyumba ya Davide.+ 1 Mafumu 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Solomo anatumiza uthenga kwa Hiramu, kuti:+
11 Ndiyeno Hiramu+ mfumu ya Turo anatumiza amithenga+ kwa Davide. Anatumizanso mitengo ya mkungudza,+ anthu a ntchito zamatabwa ndi a ntchito za miyala yomangira khoma,* ndipo anayamba kumanga nyumba ya Davide.+