Levitiko 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kuchokera pa tsiku limene sabata la 7 lakwanira, pazidutsa masiku 50,+ ndipo muzipereka nsembe yambewu zatsopano+ kwa Yehova. Machitidwe 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano pa tsiku la chikondwerero cha Pentekosite,+ onse anali atasonkhana pamalo amodzi.
16 Kuchokera pa tsiku limene sabata la 7 lakwanira, pazidutsa masiku 50,+ ndipo muzipereka nsembe yambewu zatsopano+ kwa Yehova.