Miyambo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wodala ndi munthu amene wapeza nzeru,+ ndiponso munthu amene wapeza kuzindikira,+ Miyambo 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Wodala ndi munthu amene amandimvetsera mwa kukhala maso pamakomo anga tsiku ndi tsiku, mwa kuyang’anitsitsa pamafelemu a makomo anga.+
34 Wodala ndi munthu amene amandimvetsera mwa kukhala maso pamakomo anga tsiku ndi tsiku, mwa kuyang’anitsitsa pamafelemu a makomo anga.+