Genesis 49:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yuda ndi mwana wa mkango.+ Umapha nyama n’kubwerako ndithu, mwana wanga. Iye amapinda mawondo ake n’kudziwongola ngati mkango utagona pansi. Ndipo monga mkango, ndani angamudzutse?+ Miyambo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,+ koma olungama ali ngati mkango wamphamvu umene umakhala wolimba mtima.+ Chivumbulutso 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma mmodzi wa akulu aja anandiuza kuti: “Tonthola. Taona! Mkango wa fuko la Yuda,+ muzu+ wa Davide,+ anapambana pa nkhondo+ moti iye ndiye woyenera kumatula zidindo 7 zimene amatira mpukutuwo ndi kuutsegula.”
9 Yuda ndi mwana wa mkango.+ Umapha nyama n’kubwerako ndithu, mwana wanga. Iye amapinda mawondo ake n’kudziwongola ngati mkango utagona pansi. Ndipo monga mkango, ndani angamudzutse?+
28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,+ koma olungama ali ngati mkango wamphamvu umene umakhala wolimba mtima.+
5 Koma mmodzi wa akulu aja anandiuza kuti: “Tonthola. Taona! Mkango wa fuko la Yuda,+ muzu+ wa Davide,+ anapambana pa nkhondo+ moti iye ndiye woyenera kumatula zidindo 7 zimene amatira mpukutuwo ndi kuutsegula.”