Levitiko 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musadye mkate, mbewu zokazinga kapena mbewu zatsopano kufikira tsiku limeneli,+ mpaka mutabweretsa nsembe ya Mulungu wanu. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale ku mibadwo yanu yonse, kulikonse kumene mungakhale. Levitiko 23:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Muzichitira Yehova chikondwerero chimenechi masiku 7 pa chaka,+ m’mwezi wa 7. Limeneli ndi lamulo m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.
14 Musadye mkate, mbewu zokazinga kapena mbewu zatsopano kufikira tsiku limeneli,+ mpaka mutabweretsa nsembe ya Mulungu wanu. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale ku mibadwo yanu yonse, kulikonse kumene mungakhale.
41 Muzichitira Yehova chikondwerero chimenechi masiku 7 pa chaka,+ m’mwezi wa 7. Limeneli ndi lamulo m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.