Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 10:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho mafumu asanu a Aamoriwo+ anakumana pamodzi n’kunyamuka. Mafumuwo anali: Mfumu ya ku Yerusalemu, mfumu ya ku Heburoni, mfumu ya ku Yarimuti, mfumu ya ku Lakisi, ndi mfumu ya ku Egiloni. Mafumu amenewa, pamodzi ndi magulu awo ankhondo anakamanga msasa pafupi ndi mzinda wa Gibeoni, n’cholinga chouthira nkhondo.

  • 2 Mbiri 32:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pambuyo pa zimenezi, Senakeribu+ mfumu ya Asuri ali ku Lakisi+ pamodzi ndi asilikali ake onse,+ anatumiza atumiki ake ku Yerusalemu kwa Hezekiya mfumu ya Yuda ndi kwa anthu onse okhala ku Yudeya ku Yerusalemu. Anawatuma kukanena kuti:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena