Deuteronomo 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Asachulukitsenso akazi kuti mtima wake ungapatuke,+ ndipo asachulukitsenso kwambiri siliva ndi golide wake.+ Oweruza 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Gidiyoni anakhala ndi ana 70+ otuluka m’chiuno mwake, chifukwa anadzakhala ndi akazi ambiri. 1 Mafumu 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iye anali ndi akazi olemekezeka 700, ndi akazi ena apambali 300. M’kupita kwa nthawi,+ akazi amenewa anapotoza mtima wa Solomo.
17 Asachulukitsenso akazi kuti mtima wake ungapatuke,+ ndipo asachulukitsenso kwambiri siliva ndi golide wake.+
3 Choncho iye anali ndi akazi olemekezeka 700, ndi akazi ena apambali 300. M’kupita kwa nthawi,+ akazi amenewa anapotoza mtima wa Solomo.