2 Samueli 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ngakhale kuti anali wolemekezeka kwambiri kuposa amuna ena 30 aja, sanafanane ndi amuna atatu aja. Koma Davide anamuika kukhala msilikali wake womulondera.+
23 Ngakhale kuti anali wolemekezeka kwambiri kuposa amuna ena 30 aja, sanafanane ndi amuna atatu aja. Koma Davide anamuika kukhala msilikali wake womulondera.+