Ekisodo 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Kenako upange choikapo nyale chagolide woyenga bwino. Chimenechi chikhale chosula.+ Choikapo nyalecho chikhale ndi tsinde, nthambi, masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa. Ekisodo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Koma iwe, ulamule ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale ziziyaka nthawi zonse.+ 2 Mbiri 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anapanga zoikapo nyale+ 10 zagolide zofanana,+ n’kuziika m’kachisi. Anaika zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere.+
31 “Kenako upange choikapo nyale chagolide woyenga bwino. Chimenechi chikhale chosula.+ Choikapo nyalecho chikhale ndi tsinde, nthambi, masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa.
20 “Koma iwe, ulamule ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale ziziyaka nthawi zonse.+
7 Kenako anapanga zoikapo nyale+ 10 zagolide zofanana,+ n’kuziika m’kachisi. Anaika zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere.+