1 Mafumu 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno Basa+ mwana wa Ahiya wa nyumba ya Isakara, anayamba kuchitira chiwembu Nadabu. Iye anapha Nadabu kumzinda wa Gebetoni,+ womwe unali m’manja mwa Afilisiti, pa nthawi imene Nadabu ndi Aisiraeli onse anali kuukira Gebetoni.
27 Ndiyeno Basa+ mwana wa Ahiya wa nyumba ya Isakara, anayamba kuchitira chiwembu Nadabu. Iye anapha Nadabu kumzinda wa Gebetoni,+ womwe unali m’manja mwa Afilisiti, pa nthawi imene Nadabu ndi Aisiraeli onse anali kuukira Gebetoni.