Yoswa 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Palibe amene adzatha kulimbana nawe masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe+ monga mmene ndinakhalira ndi Mose, sindidzakutaya kapena kukusiya ngakhale pang’ono.+ 1 Mbiri 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Kodi Yehova Mulungu wanu sali nanu?+ Kodi sanakupatseni mpumulo m’dziko lonseli?+ Pakuti iye wapereka m’manja mwanga anthu a m’dzikoli, ndipo dzikoli lagonjetsedwa pamaso pa Yehova+ ndi pa anthu ake. Salimo 46:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.] Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
5 Palibe amene adzatha kulimbana nawe masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe+ monga mmene ndinakhalira ndi Mose, sindidzakutaya kapena kukusiya ngakhale pang’ono.+
18 “Kodi Yehova Mulungu wanu sali nanu?+ Kodi sanakupatseni mpumulo m’dziko lonseli?+ Pakuti iye wapereka m’manja mwanga anthu a m’dzikoli, ndipo dzikoli lagonjetsedwa pamaso pa Yehova+ ndi pa anthu ake.
7 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.]
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+