8 Tsopano kwa nthawi yochepa, Yehova Mulungu wathu watikomera mtima+ mwa kutisiyira anthu opulumuka,+ ndiponso mwa kutipatsa malo otetezeka* m’malo ake oyera kuti maso athu awale,+ inu Mulungu wathu, ndi kutitsitsimutsa pang’ono mu ukapolo wathu.+
2 Ndiyeno Haneni+ mmodzi mwa abale anga anabwera pamodzi ndi amuna ena kuchokera ku Yuda. Ndinawafunsa+ mmene zinthu zinalili kwa gulu la Ayuda+ amene anathawa+ ku ukapolo+ komanso ndinawafunsa za Yerusalemu.