Ezara 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Tsopano ngati inu mfumu mukuona kuti n’koyenera, uzani anthu afufuze+ m’nyumba ya chuma cha mfumu imene ili ku Babuloko, kuti aone ngati mfumu Koresi inaikadi lamulo+ loti nyumba ya Mulungu yomwe ili ku Yerusalemu imangidwenso. Inu mfumu mutitumizire chigamulo chanu pankhani imeneyi.” Ezara 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ineyo mfumu Aritasasita ndalamula+ asungichuma onse+ amene ali kutsidya lina la Mtsinje,*+ kuti chilichonse chimene wansembe Ezara,+ wokopera chilamulo cha Mulungu wakumwamba, angapemphe kwa inu chichitidwe mwamsanga.
17 “Tsopano ngati inu mfumu mukuona kuti n’koyenera, uzani anthu afufuze+ m’nyumba ya chuma cha mfumu imene ili ku Babuloko, kuti aone ngati mfumu Koresi inaikadi lamulo+ loti nyumba ya Mulungu yomwe ili ku Yerusalemu imangidwenso. Inu mfumu mutitumizire chigamulo chanu pankhani imeneyi.”
21 “Ineyo mfumu Aritasasita ndalamula+ asungichuma onse+ amene ali kutsidya lina la Mtsinje,*+ kuti chilichonse chimene wansembe Ezara,+ wokopera chilamulo cha Mulungu wakumwamba, angapemphe kwa inu chichitidwe mwamsanga.