Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 36:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 M’chaka choyamba cha Koresi+ mfumu ya Perisiya,+ Yehova analimbikitsa mtima+ wa Koresi mfumu ya Perisiya kuti mawu a Yehova+ kudzera mwa Yeremiya+ akwaniritsidwe. Pamenepo Koresiyo anatumiza mawu amene analengezedwa mu ufumu wake wonse. Mawuwo analembedwanso m’makalata,+ kuti:

  • Ezara 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Aliyense amene ali pakati panu mwa anthu onse amene amamutumikira, Mulungu wake akhale naye.+ Choncho apite ku Yerusalemu m’dziko la Yuda n’kukamanganso nyumba ya Yehova Mulungu wa Isiraeli, yomwe inali ku Yerusalemu.+ Iye ndiye Mulungu woona.+

  • Ezara 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “M’chaka choyamba cha Mfumu Koresi,+ mfumuyo inaika lamulo lokhudza nyumba ya Mulungu ku Yerusalemu lakuti: Ayuda amangenso nyumbayo kuti azikapereka nsembe+ kumeneko, ndipo amange maziko olimba. Nyumbayo kutalika kwake kuchokera pansi kufika pamwamba ikhale mikono* 60, ndiponso m’lifupi mwake ikhale mikono 60.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena