2 Mafumu 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu ena onse amene anatsala mumzindamo, ndi anthu amene anapita kumbali ya mfumu ya Babulo, ndiponso anthu ena onse,+ Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anawatenga kupita nawo ku ukapolo.+
11 Anthu ena onse amene anatsala mumzindamo, ndi anthu amene anapita kumbali ya mfumu ya Babulo, ndiponso anthu ena onse,+ Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anawatenga kupita nawo ku ukapolo.+