Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 39:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu,+ anatenga anthu ena onse otsala mumzindamo, anthu amene anathawira kwa mfumu ya Babulo ndi anthu ena onse amene anapulumuka kupita nawo ku ukapolo ku Babulo.+

  • Yeremiya 52:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 M’chaka cha 23 cha ulamuliro wa Nebukadirezara, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga Ayuda 745 kupita nawo ku ukapolo.+

      Anthu onse amene anawatenga anali 4,600.

  • Ezekieli 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndikadzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndi kumayiko ena, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+

  • Ezekieli 22:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Anthu ako ndidzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndipo ndidzawamwaza m’mayiko osiyanasiyana.+ Komanso ndidzachotsa zodetsa zako mwa iwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena