Deuteronomo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipo Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo mudzatsala ochepa+ m’mayiko a mitundu imene Yehova adzakuingitsiraniko. Deuteronomo 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova adzakuchititsani kuti mugonje pamaso pa adani anu.+ Pokamenyana nawo nkhondo mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pawo mudzadutsa njira 7. Mudzakhala chinthu chonyansa kwa mafumu onse a dziko lapansi.+ Ezekieli 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndikadzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndi kumayiko ena, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
27 Ndipo Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo mudzatsala ochepa+ m’mayiko a mitundu imene Yehova adzakuingitsiraniko.
25 Yehova adzakuchititsani kuti mugonje pamaso pa adani anu.+ Pokamenyana nawo nkhondo mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pawo mudzadutsa njira 7. Mudzakhala chinthu chonyansa kwa mafumu onse a dziko lapansi.+
15 Ndikadzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndi kumayiko ena, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+