Ekisodo 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mkate wopanda chofufumitsa, mkate wozungulira woboola pakati, wopanda chofufumitsa, wothira mafuta ndi timitanda ta mkate topyapyala topanda chofufumitsa, topaka mafuta.+ Uzipange ndi ufa wa tirigu wosalala. Levitiko 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo.
2 mkate wopanda chofufumitsa, mkate wozungulira woboola pakati, wopanda chofufumitsa, wothira mafuta ndi timitanda ta mkate topyapyala topanda chofufumitsa, topaka mafuta.+ Uzipange ndi ufa wa tirigu wosalala.
2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo.