Ekisodo 29:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku nthawi zonse.+ Numeri 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Uwauze kuti, ‘Muzipereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto motere: Tsiku lililonse muzipereka nsembe yopsereza ya ana a nkhosa awiri amphongo, achaka chimodzi ndi opanda chilema.+
38 “Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku nthawi zonse.+
3 “Uwauze kuti, ‘Muzipereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto motere: Tsiku lililonse muzipereka nsembe yopsereza ya ana a nkhosa awiri amphongo, achaka chimodzi ndi opanda chilema.+