18 Chotero, popeza dzanja labwino+ la Mulungu wathu linali pa ife, iwo anatibweretsera munthu wanzeru+ wochokera pakati pa ana a Mali+ mdzukulu wa Levi+ mwana wa Isiraeli, dzina lake Serebiya+ pamodzi ndi ana ake ndi abale ake. Onse pamodzi analipo 18.