Ezara 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano ndinapatula anthu 12 kuchokera pa atsogoleri a ansembe. Mayina awo anali Serebiya+ ndi Hasabiya+ pamodzi ndi abale awo 10.
24 Tsopano ndinapatula anthu 12 kuchokera pa atsogoleri a ansembe. Mayina awo anali Serebiya+ ndi Hasabiya+ pamodzi ndi abale awo 10.