-
Deuteronomo 17:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Zimene akuuza kumalo amene Yehova adzasankhe uzichita zomwezo. Uzionetsetsa kuti ukuchita zonse zimene akulangiza.
-