1 Mafumu 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mwana wake ndidzam’patsa fuko limodzi kuti Davide mtumiki wanga apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mu Yerusalemu,+ mzinda umene ndausankha kuti ndiikepo dzina langa.+
36 Mwana wake ndidzam’patsa fuko limodzi kuti Davide mtumiki wanga apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mu Yerusalemu,+ mzinda umene ndausankha kuti ndiikepo dzina langa.+