Ezara 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa ana a Elamu+ panali Yesaiya mwana wa Ataliya. Iye anali ndi amuna 70. Ezara 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa ana a Elamu+ panali Mataniya, Zekariya, Yehiela,+ Abidi, Yeremoti ndi Eliya. Nehemiya 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Elamu,+ 1,254.