Ezara 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Elamu,+ 1,254. Ezara 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa ana a Elamu+ panali Yesaiya mwana wa Ataliya. Iye anali ndi amuna 70. Nehemiya 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atsogoleri awa a anthu anatsimikiziranso panganoli: Parosi, Pahati-mowabu,+ Elamu, Zatu, Bani,