2 Mbiri 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anayamba kuphunzitsa+ mu Yuda pogwiritsira ntchito buku la chilamulo cha Yehova.+ Ankayendayenda m’mizinda yonse ya Yuda n’kumaphunzitsa anthu.
9 Iwo anayamba kuphunzitsa+ mu Yuda pogwiritsira ntchito buku la chilamulo cha Yehova.+ Ankayendayenda m’mizinda yonse ya Yuda n’kumaphunzitsa anthu.