Salimo 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndilangizeni, inu Yehova, kuti ndiyende m’njira yanu.+Nditsogolereni m’njira yowongoka kuti nditetezeke kwa adani anga. Yesaya 30:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Makutu ako adzamva mawu kumbuyo kwako, akuti: “Njira ndi iyi.+ Yendani mmenemu anthu inu.” Yendani m’njira imeneyi kuti musasochere n’kulowera kudzanja lamanja kapena lamanzere.+
11 Ndilangizeni, inu Yehova, kuti ndiyende m’njira yanu.+Nditsogolereni m’njira yowongoka kuti nditetezeke kwa adani anga.
21 Makutu ako adzamva mawu kumbuyo kwako, akuti: “Njira ndi iyi.+ Yendani mmenemu anthu inu.” Yendani m’njira imeneyi kuti musasochere n’kulowera kudzanja lamanja kapena lamanzere.+