Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ziwiya+ zimene ukupatsidwa kuti zikagwiritsidwe ntchito pa utumiki wa panyumba ya Mulungu wako, ukazipereke zonse ku Yerusalemu n’kukaziika pamaso pa Mulungu.+

  • Ezara 8:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Pa tsiku lachinayi tinayeza siliva, golide+ ndi ziwiya+ zija m’nyumba ya Mulungu wathu. Titatero tinapereka zinthuzo m’manja mwa wansembe Meremoti+ mwana wa Uliya, yemwe anali limodzi ndi Eleazara mwana wa Pinihasi. Iwowa anali limodzi ndi Yozabadi+ mwana wa Yesuwa ndi Nowadiya mwana wa Binui,+ omwe anali Alevi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena