Yoswa 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kunalinso Gibeoni,+ Rama, Beeroti, 1 Mafumu 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho Basa mfumu ya Isiraeli anapita kukaukira Yuda. Kenako anayamba kumanga mpanda wolimba kwambiri kuzungulira mzinda wa Rama,+ kuti anthu asamapite kwa Asa mfumu ya Yuda kapena kubwera kuchokera kwa Asa.+ Nehemiya 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Amuna a ku Rama+ ndi ku Geba,+ 621. Nehemiya 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Hazori, Rama,+ Gitaimu,+
17 Choncho Basa mfumu ya Isiraeli anapita kukaukira Yuda. Kenako anayamba kumanga mpanda wolimba kwambiri kuzungulira mzinda wa Rama,+ kuti anthu asamapite kwa Asa mfumu ya Yuda kapena kubwera kuchokera kwa Asa.+