1 Mafumu 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu awa akapitiriza kupita kukapereka nsembe kunyumba ya Yehova ku Yerusalemu,+ mtima wawo ubwerera kwa mbuye wawo Rehobowamu mfumu ya Yuda, ndipo ineyo adzandipha+ n’kubwerera kwa Rehobowamu mfumu ya Yuda.” 2 Mbiri 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aleviwo anasiya malo awo odyetserako ziweto+ ndi madera awo+ n’kupita ku Yuda ndi ku Yerusalemu,+ chifukwa Yerobowamu+ ndi ana ake anachotsa+ Aleviwo pa udindo wokhala ansembe a Yehova.
27 Anthu awa akapitiriza kupita kukapereka nsembe kunyumba ya Yehova ku Yerusalemu,+ mtima wawo ubwerera kwa mbuye wawo Rehobowamu mfumu ya Yuda, ndipo ineyo adzandipha+ n’kubwerera kwa Rehobowamu mfumu ya Yuda.”
14 Aleviwo anasiya malo awo odyetserako ziweto+ ndi madera awo+ n’kupita ku Yuda ndi ku Yerusalemu,+ chifukwa Yerobowamu+ ndi ana ake anachotsa+ Aleviwo pa udindo wokhala ansembe a Yehova.