5 koma mudzafunefune malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe pakati pa mafuko anu onse kuti aikepo dzina lake, kuti lizikhala pamenepo. Amenewo ndiwo malo amene muzidzapitako.+
32 Fuko limodzi+ lipitiriza kukhala lake chifukwa cha mtumiki wanga Davide,+ ndiponso chifukwa cha mzinda wa Yerusalemu+ umene ndausankha pa mafuko onse a Isiraeli.