Genesis 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+ 1 Mafumu 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Kunena za nyumba ukumangayi, ukayenda motsatira malamulo+ anga ndi kusunga zigamulo+ zanga zonse ndi kuzitsatira,+ inenso ndidzakwaniritsadi mawu anga okhudza iweyo amene ndinalankhula kwa bambo ako Davide.+ 1 Mafumu 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aisiraeli onse atangomva kuti Yerobowamu wabwera, nthawi yomweyo anatumiza uthenga womuitanira kumene anasonkhana, ndipo anamuika kukhala mfumu ya Aisiraeli onse.+ Palibenso amene ankatsatira nyumba ya Davide kupatula fuko la Yuda lokha.+
10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+
12 “Kunena za nyumba ukumangayi, ukayenda motsatira malamulo+ anga ndi kusunga zigamulo+ zanga zonse ndi kuzitsatira,+ inenso ndidzakwaniritsadi mawu anga okhudza iweyo amene ndinalankhula kwa bambo ako Davide.+
20 Aisiraeli onse atangomva kuti Yerobowamu wabwera, nthawi yomweyo anatumiza uthenga womuitanira kumene anasonkhana, ndipo anamuika kukhala mfumu ya Aisiraeli onse.+ Palibenso amene ankatsatira nyumba ya Davide kupatula fuko la Yuda lokha.+