Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 koma sindidzauchotsa wonse.+ Ndidzapereka fuko limodzi kwa mwana wako, chifukwa cha Davide mtumiki wanga+ ndiponso chifukwa cha Yerusalemu, mzinda umene ndausankha.”+

  • 2 Mbiri 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma ife, Yehova ndiye Mulungu wathu+ ndipo sitinamusiye. Ansembe, omwe ndi ana a Aroni, akutumikira Yehova, ndiponso Alevi akugwira ntchito yawo.+

  • 2 Mbiri 25:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako Amaziya anasonkhanitsa Ayuda n’kuwaimiritsa motsatira nyumba ya makolo awo.+ Anawaika m’magulu a anthu 1,000+ ndi mtsogoleri wawo, ndiponso m’magulu a anthu 100+ ndi mtsogoleri wawo, a mafuko a Yuda ndi Benjamini. Iye anawalemba mayina anthuwo, kuyambira azaka 20+ kupita m’tsogolo ndipo anapeza kuti analipo 300,000. Anali amuna ochita kusankhidwa a m’gulu la asilikali, onyamula mkondo waung’ono+ ndi chishango chachikulu.+

  • Hoseya 11:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Efuraimu amalankhula mabodza okhaokha kwa ine.+ Kulikonse kumene ndingayang’ane ndikuona chinyengo cha Isiraeli, koma Yuda akuyendabe ndi Mulungu+ ndipo iye ndi wokhulupirika kwa Woyera Koposa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena