2 Samueli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachoka pa iye monga mmene ndinakuchotsera pa Sauli,+ amene ndinam’chotsa pamaso pako. 1 Mbiri 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Sindidzachotsa kukoma mtima kwanga kosatha pa iye+ monga mmene ndinachitira kwa amene analipo iwe usanakhalepo.+ Salimo 89:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma kukoma mtima kwanga kosatha sindidzakuchotsa pa iye,+Ndipo sindidzasiya kukhulupirika kwanga.+
15 Ndipo kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachoka pa iye monga mmene ndinakuchotsera pa Sauli,+ amene ndinam’chotsa pamaso pako.
13 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Sindidzachotsa kukoma mtima kwanga kosatha pa iye+ monga mmene ndinachitira kwa amene analipo iwe usanakhalepo.+
33 Koma kukoma mtima kwanga kosatha sindidzakuchotsa pa iye,+Ndipo sindidzasiya kukhulupirika kwanga.+