2 Samueli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachoka pa iye monga mmene ndinakuchotsera pa Sauli,+ amene ndinam’chotsa pamaso pako. 1 Mafumu 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Fuko limodzi+ lipitiriza kukhala lake chifukwa cha mtumiki wanga Davide,+ ndiponso chifukwa cha mzinda wa Yerusalemu+ umene ndausankha pa mafuko onse a Isiraeli. 1 Mafumu 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mwana wake ndidzam’patsa fuko limodzi kuti Davide mtumiki wanga apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mu Yerusalemu,+ mzinda umene ndausankha kuti ndiikepo dzina langa.+
15 Ndipo kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachoka pa iye monga mmene ndinakuchotsera pa Sauli,+ amene ndinam’chotsa pamaso pako.
32 Fuko limodzi+ lipitiriza kukhala lake chifukwa cha mtumiki wanga Davide,+ ndiponso chifukwa cha mzinda wa Yerusalemu+ umene ndausankha pa mafuko onse a Isiraeli.
36 Mwana wake ndidzam’patsa fuko limodzi kuti Davide mtumiki wanga apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mu Yerusalemu,+ mzinda umene ndausankha kuti ndiikepo dzina langa.+