Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno malo+ amene Yehova Mulungu wanu adzasankha kuti pakhale dzina lake n’kumene muzidzabweretsa zonse zimene ndikukulamulani, nsembe zanu zopsereza+ ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,+ chopereka+ chochokera m’manja mwanu ndi zonse zimene mwasankha kukhala nsembe zanu za lonjezo,+ zimene mudzalonjeza Yehova.

  • 1 Mafumu 11:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Fuko limodzi+ lipitiriza kukhala lake chifukwa cha mtumiki wanga Davide,+ ndiponso chifukwa cha mzinda wa Yerusalemu+ umene ndausankha pa mafuko onse a Isiraeli.

  • Yesaya 60:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena