1 Mbiri 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Elipaala anali Ebere, Misamu, ndi Semedi. Semedi ndiye anamanga mzinda wa Ono+ ndiponso mzinda wa Lodi,+ ndi midzi yake yozungulira. Nehemiya 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Lodi,+ Ono+ ndi kuchigwa cha amisiri.
12 Ana a Elipaala anali Ebere, Misamu, ndi Semedi. Semedi ndiye anamanga mzinda wa Ono+ ndiponso mzinda wa Lodi,+ ndi midzi yake yozungulira.