Nehemiya 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atsogoleri+ a kumeneko sanadziwe kumene ndapita ndi zimene ndinali kuchita. Komanso Ayuda pamodzi ndi ansembe, anthu olemekezeka, atsogoleri ndi ena onse amene akanagwira ntchito yomanga mpanda ndinali ndisanawauze kalikonse. Nehemiya 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ndinayamba kuimba mlandu anthu olemekezeka+ a ku Yuda kuti: “N’chifukwa chiyani mukuchita zinthu zoipa, mpaka kuipitsa tsiku la sabata?
16 Atsogoleri+ a kumeneko sanadziwe kumene ndapita ndi zimene ndinali kuchita. Komanso Ayuda pamodzi ndi ansembe, anthu olemekezeka, atsogoleri ndi ena onse amene akanagwira ntchito yomanga mpanda ndinali ndisanawauze kalikonse.
17 Choncho ndinayamba kuimba mlandu anthu olemekezeka+ a ku Yuda kuti: “N’chifukwa chiyani mukuchita zinthu zoipa, mpaka kuipitsa tsiku la sabata?